3 John 1:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono ife tiyenera kumaŵathandiza anthu otere, kuti tigwirizane nawo pa ntchito yofalitsa choona.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake ife tiyenera kulandira otere, kuti tikakhale othandizana nacho choonadi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ife tiyenera kumathandiza anthu oterewa, kuti tigwirizane nawo pa ntchito ya choonadi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace ife tiyenera kulandira otere, kuti tikakhale othandizana naco coonadi,