3 John 1:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndidalembera mpingo mau pang'ono, koma Diotrefe safuna kundimvera. Iye amafuna kukhala mtsogoleri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndalemba kanthu kwa Mpingo; komatu Diotrefe uja, wofuna kukhala wamkulu wa iwo, satilandira ife.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndinalembera mpingo, koma Diotrefe, amene amafuna kukhala wotsogolera, sanafune kutimvera.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndalemba kanthu kwa Mpingo; komatu Diotrefe uja, wofuna kukhala wamkuru wa iwo, satilandira ife.