Acts 1:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yudasiyo anali mmodzi wa gulu lathu, ndipo adaalandira udindo woti azitumikira pamodzi ndi ife.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa anali wowerengedwa mwa ife, ndipo analandira gawo lake la utumiki uwu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anali mmodzi wa gulu lathu ndipo anatumikira pamodzi ndi ife.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa anali wowerengedwa mwa ife, ndipo analandira gawo lace la utumiki uwu.