Acts 10:16 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zimenezi zidachitika katatu, ndipo pompo chinthu chija chidatengedwa kupitanso kumwamba.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo chinachitika katatu ichi; ndipo pomwepo chotengeracho chinatengedwa kunka kumwamba.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zimenezi zinachitika katatu ndipo nthawi yomweyo chinsalu chija chinatengedwanso kupita kumwamba.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo cinacitika katatu ici; ndipo pomwepo cotengeraco cinatengedwa kunka kumwamba.