Acts 10:18 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adaitana nkufunsa kuti, “Kodi kuli mlendo kuno, dzina lake Simoni, wotchedwanso Petro?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo anaitana nafunsa ngati Simoni, wotchedwanso Petro, acherezedwako.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo anayitana nafunsa ngati Simoni amene amadziwika ndi dzina loti Petro amakhala kumeneko.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo anaitana nafunsa ngati Simoni, wochedwanso Petro, acerezedwako.