Acts 10:21 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Apo Petro adatsika nauza anthu aja kuti, “Amene mukumfunayo ndine. Kodi nkwabwino?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Petro anatsikira kwa anthuwo, nati, Taonani, ine ndine amene mumfuna; chifukwa chake mwadzera nchiyani?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Petro anatsika ndipo anati kwa anthuwo, “Amene mukufunayo ndine. Mwabwera kuno chifukwa chiyani?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Petro anatsikira kwa anthuwo, nati, Taonani, ine ndine amene mumfuna; cifukwa cace mwadzera nciani?