Acts 10:35 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amalandira bwino munthu wa mtundu uliwonse womuwopa nkumachita chilungamo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
koma m'mitundu yonse, wakumuopa Iye ndi wakuchita chilungamo alandiridwa naye.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma amalandira anthu a mtundu uli wonse amene amaopa Iye ndiponso kuchita chilungamo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
koma m'mitundu yonse, wakumuopa iye ndi wakucita cilungamo alandiridwa naye.