Acts 11:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zimenezi zidachitika katatu, ndipo zonsezo zinatengedwa kupitanso kumwamba.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ichi chinachitika katatu; ndipo zinakwezekanso zonse kumwamba.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zimenezi zinachitika katatu ndipo kenaka zonse zinatengedwa kupita kumwamba.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ici cinacitika katatu; ndipo zinakwezekanso zonse kumwamba.