Acts 11:30 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zimenezi adachitadi, ndipo anatuma Barnabasi ndi Saulo kukapereka thandizolo kwa akulu a mpingo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ichonso anachita, natumiza kwa akulu mwa dzanja la Barnabasi ndi Saulo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Izi anazichitadi ndipo anatuma Barnaba ndi Saulo kukapereka mphatsozo kwa akulu a mpingo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
iconso anacita, natumiza kwa akulu mwa dzanja la Bamaba ndi Saulo.