Acts 11:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma mau ochokera kumwamba aja adanenanso kachiŵiri kuti, ‘Zimene Mulungu waziyeretsa, iwe usati nzosayera.’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma mau anayankha nthawi yachiwiri otuluka m'mwamba, Chimene Mulungu anachiyeretsa, usachiyesera chinthu wamba.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Mawu ochokera kumwamba ananenanso kachiwiri kuti, ‘Chimene Mulungu wachiyeretsa usanene kuti ndi chodetsedwa.’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma mau anayankha nthawi yaciwiri oturuka m'mwamba, Cimene Mulungu anaciyeretsa, usaciyesera cinthu wamba.
Recommended Reading