Acts 12:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthuwo adati, “Wapenga iwe!” Koma iye adalimbikira kuti nzoonadi. Apo iwo adati, “Ndi mngelo wake ameneyo.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma anati kwa iye, Wamisala iwe. Ndipo analimbika ndi kunena kuti nkutero. Ndipo ananena, Ndiye mngelo wake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthuwo anati kwa iye, “Wopenga iwe!” Atalimbikira kunena kuti zinali zoona, iwo anati, “Ameneyo ndi mngelo wake.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma anati kwa iye, Wamisala iwe. Ndipo analimbika ndi kunena kuti nkutero. Ndipo ananena, Ndiye mngelo wace.