Acts 12:16 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Petro ankangogogodabe. Pamene adamtsekulira nkuwona kuti ndiyedi, adangoti kakasi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma Petro anakhala chigogodere; ndipo m'mene adamtsegulira, anamuona iye, nadabwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Petro anapitiriza kugogoda ndipo atatsekula chitseko ndi kumuona, anthuwo anadabwa kwambiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma Petro anakhala cigogodere; ndipo m'mene adamtsegulira, anamuona iye, nadabwa.