Acts 12:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kutacha, asilikali aja adasokonezeka kwabasi nati, “Petro wapita kuti?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma kutacha, panali phokoso lalikulu mwa asilikali, Petro wamuka kuti.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamene kunacha kunali phokoso lalikulu pakati pa asilikali, iwo anafunsa kuti, “Kodi chamuchitikira Petro ndi chiyani?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma kutaca, panali phokoso lalikuru mwa asilikari, Petro wamuka kuti.