Acts 13:16 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Apo Paulo adaimirira nakweza dzanja kuti anthu akhale chete, ndipo adayamba kulankhula. Adati, “Inu Aisraele, ndi ena nonse oopa Mulungu, mverani.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Paulo ananyamuka, nakodola ndi dzanja, nati, Amuna a Israele, ndi inu akuopa Mulungu, mverani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Atayimirira, Paulo anakweza dzanja lake ndi kuti, “Inu Aisraeli ndiponso inu a mitundu ina amene mumapembedza Mulungu, tandimverani!
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Paulo ananyamuka, nakodola ndi dzanja, nati, Amuna a Israyeli, ndi inu akuopa Mulungu, mverani.