Acts 13:24 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iyeyo asanayambe ntchito, Yohane ankalalikira Aisraele onse kuti atembenuke mtima ndi kubatizidwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yohane atalalikiratu, asanafike Iye, ubatizo wa kulapa kwa anthu onse a Israele.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yesu asanabwere, Yohane analalikira kwa anthu onse Aisraeli za kutembenuka mtima ndi ubatizo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yohane atalalikiratu, asanafike iye, ubatizo wa kulapa kwa anthu onse a Israyeli.