Acts 13:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono atasala zakudya ndi kupemphera adaŵasanjika manja naŵatuma.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo, m'mene adasala chakudya ndi kupemphera ndi kuika manja pa iwo, anawatumiza amuke.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo atasala kudya ndi kupemphera anasanjika manja awo pa iwo nawatumiza.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo, m'mene adasala cakudya ndi kupemphera ndi kuika manja pa iwo, anawatumiza amuke.