Acts 13:32 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo ife tikukulalikirani Uthenga Wabwino wakuti zilipo zimene Mulungu adaaŵalonjeza makolo athu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ife tikulalikirani inu Uthenga Wabwino wa lonjezano lochitidwa kwa makolo;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Ife tikukuwuzani Uthenga Wabwino; umene Mulungu analonjeza makolo athu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ife tikulalikirani inu Uthenga Wabwino wa 2 lonjezano locitidwa kwa makolo;