Acts 13:33 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono zimene adaalonjezazo Iye watichitire ifeyo, zidzukulu zao, pakuukitsa Yesu kwa akufa. Monganso mudalembedwera m'Salimo lachiŵiri kuti, “ ‘Iwe ndiwe Mwana wanga, Ine lero ndakubala.’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kuti Mulungu analikwaniritsa ili kwa ana athu pakuukitsa Yesu; monganso mulembedwa m'Salimo lachiwiri, Iwe ndiwe Mwana wanga, lero ndakubala.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye wakwaniritsa zimenezi kwa ife ana awo, poukitsa Yesu kuchokera kwa akufa. Monga zinalembedwa mu Salimo lachiwiri kuti, “Iwe ndiwe mwana wanga; lero ine ndakhala Atate ako.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
kuti Mulungu analikwaniritsa ili kwa ana athu pakuukitsa Yesu; monganso mulembedwa m'Salmo laciwiri, Iwe ndiwe Mwana wanga, lero ndakubala.