Acts 13:35 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nchifukwa chake m'Salimo lina akutinso, “ ‘Simudzalekerera Woyera wanu kuti aole.’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa anenanso m'Salimo lina, Simudzapereka Woyera wanu aone chivundi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nʼchifukwa chakenso zinalembedwa mu Salimo lina kuti, “ ‘Simudzalekerera woyera wanu kuti awole.’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa anenanso m'Salmo lina, 4 Simudzapereka Woyera wanu aone cibvundi.