Acts 13:40 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndiye inu chenjerani kuti zingakugwereni zimene aneneri aja adanena kuti,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake penyerani, kuti chingadzere inu chonenedwa ndi aneneriwo:
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Samalani kuti zimene aneneri akunena zisakuchitikireni inu:
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace penyerani, kuti cingadzere inu conenedwa ndi anenenwo: