Acts 13:41 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“ ‘Mvetsani inu anthu onyoza, zizwani ndipo muwonongeke, pakuti pa nthaŵi ya moyo wanu Ine ndidzachita chinthu chimene simungakhulupirire konse, ngakhale wina akuuzeni.’ ”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Taonani, opeputsa inu, zizwani, kanganukani; kuti ndigwiritsa ntchito Ine masiku anu, ntchito imene simudzaikhulupirira wina akakuuzani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“ ‘Onani, inu anthu onyoza, dabwani ndipo wonongekani, chifukwa ine ndidzachita china chake mʼmasiku anu, inu simudzazikhulupirira ngakhale wina atakufotokozerani!’ ”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
7 Taona ni, opeputsa inu, zizwani, kanganukani; Kuti ndigwiritsa nchito Ine masikuanu, Nchito imene simudzaikhulupira wina akakuuzani.