Acts 13:42 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene ankatuluka, anthu aja adapempha Paulo ndi Barnabasi kuti adzaŵakambirenso zomwezi tsiku la Sabata linalo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo pakutuluka iwo anapempha kuti alankhule naonso mau awa Sabata likudzalo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamene Paulo ndi Barnaba amatuluka mʼSunagoge, anthu anawapempha kuti adzapitirize kuyankhula zinthu zimenezi Sabata linalo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo pakuturuka iwo anapempha kuti alankhule naonso mau awa Sabata likudzalo.