Acts 13:47 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Paja Ambuye adatilamula kuti, “ ‘Ndakuika kuti uunikire anthu akunja, kuti mwa iwe ndipulumutse dziko lonse lapansi.’ ”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti kotero anatilamula Ambuye ndi kuti, Ndakuika iwe kuunika kwa amitundu, kuti udzakhala iwe chipulumutso kufikira malekezero a dziko.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti izi ndi zimene Ambuye anatilamula ife: “ ‘Ine ndakuyika iwe ukhale kuwunika kwa anthu a mitundu ina, kuti ukafikitse chipulumutso ku malekezero a dziko lapansi!’ ”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti kotero anatilamulira Ambuye ndi kuti, 11 Ndakuika iwe kuunika kwa amitundu, Kuti udzakhala iwe cipulumutso kufikira malekezero a dziko.