Acts 13:51 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma iwo adasansa fumbi la kumapazi kwao moŵatsutsa, napita ku Ikonio.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma iwo, m'mene adawasansira fumbi la ku mapazi ao anadza ku Ikonio.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono iwo anasasa fumbi la ku mapazi awo powatsutsa, ndipo anapita ku Ikoniya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma iwo, 13 m'mene adawasansirapfumbi la ku mapazi ao anadza ku Ikoniyo,