Acts 14:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ngakhale ndi mau ameneŵa, adavutika kuŵaletsa anthu aja kuti asaŵaphere nsembe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakunena izo, anavutika pakuletsa makamu kuti asapereke nsembe kwa iwo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngakhale ndi mawu awa, anavutika kuletsa gulu la anthu kuti asapereke nsembe kwa iwo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakunena izo, anabvutika pakuletsa makamu kuti asapereke nsembe kwa iwo.