Acts 14:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Ayuda amene sadakhulupirire adautsa mitima ya akunjawo kuti adane ndi akhristu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma Ayuda osamvera anautsa mitima ya Agriki kuti aipse abale athu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Ayuda amene anakana kukhulupirira anawutsa anthu a mitundu ina nawononga maganizo awo kutsutsana ndi abale.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma Ayuda osamvefa anautsa mitima ya Ahelene kuti aipse abale athu.