Acts 14:20 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma ophunzira ena atasonkhana nkumzungulira, iye adauka naloŵanso mumzindamo. M'maŵa mwake iye ndi Barnabasi adapita ku Deribe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma pamene anamzinga ophunzirawo, anauka iye, nalowa m'mudzi; m'mawa mwake anatuluka ndi Barnabasi kunka ku Deribe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma ophunzira atamuzungulira, Pauloyo anayimirira nalowanso mu mzindawo. Mmawa mwake iye ndi Barnaba anachoka ndi kupita ku Derbe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma pamene, anamzinga akuphunzirawo, anauka iye, nalowa m'mudzi; m'mawa mwace anaturuka ndi Bamaba kunka, ku Derbe.