Acts 14:21 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Paulo ndi Barnabasi atalalika Uthenga Wabwino ku Deribe kuja, ndi kukopa okhulupirira ambiri, adabwerera ku Listara, ku Ikonio ndi ku Antiokeya m'dera la Pisidiya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamene analalikira Uthenga Wabwino pamudzipo, nayesa ambiri ophunzira, anabwera ku Listara ndi Ikonio ndi Antiokeya,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo analalikira Uthenga Wabwino mu mzindawo ndipo anthu ambiri anatembenuka mtima ndi kukhala ophunzira. Kenaka anabwerera ku Lusitra, ku Ikoniya ndi ku Antiokeya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamene analalikira Uthenga Wabwino pamudzipo, nayesa ambiri akuphunzira, anabwera ku Lustra ndi Ikoniyo ndi Antiokeya,