Acts 14:26 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kumeneko adaloŵa m'chombo kupita ku Antiokeya kuja, kumene adaaperekedwa kwa Mulungu kuti aŵadalitse pa ntchito imene tsopano anali ataitsiriza.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
komweko anachoka m'ngalawa kunka ku Antiokeya, kumene anaikizidwa ku chisomo cha Mulungu ku ntchito imene adaimalizayo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ku Ataliyako, anakwera sitima ya pamadzi kubwerera ku Antiokeya kumene anayitanidwa mwachisomo cha Mulungu kuti agwire ntchito imene tsopano anali atayitsiriza.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
komweko anacoka m'ngalawa kunka ku Antiokeya, kumene anaikizidwa ku cisomo ca Mulungu ku Ilchito imene adaimarizayo,