Acts 14:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma anthu amumzindamo adagaŵikana, ena anali mbali ya Ayuda, ena anali mbali ya atumwi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo khamu la mudziwo linagawikana; ena anali ndi Ayuda, koma ena anali ndi atumwi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu a mu mzindamo anagawikana; ena anali mbali ya Ayuda, ena mbali ya atumwi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo khamu la mudziwo linagawikana; ena analindi Ayuda, komaena anali ndi atumwi.