Acts 14:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamenepo anthu akunja ndi Ayuda, pamodzi ndi akulu ao, adatsimikiza zoŵazunza ndi kuŵaponya miyala.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo pamene panakhala chigumukiro cha Agriki ndi cha Ayuda ndi akulu ao, cha kuwachitira chipongwe ndi kuwaponya miyala,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamenepo anthu a mitundu ina ndi Ayuda, pamodzi ndi atsogoleri awo anakonza chiwembu choti azunze atumwiwo ndi kuwagenda ndi miyala.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo pamene panakhala cigumukiro ca Ahelene ndi ca Ayuda ndi akuru ao, ca kuwacitira cipongwe ndi kuwaponya miyala,