Acts 14:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Atumwi aja atamva zimenezi, adathaŵira ku Listara ndi ku Deribe, mizinda ya ku Likaoniya, ndiponso ku dziko lozungulira mizindayo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
iwo anamva, nathawira kumidzi ya Likaoniya, Listara ndi Deribe, ndi dziko lozungulirapo:
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma atazindikira zimenezi, anathawira ku Lusitra ndi Derbe, mizinda ya ku Lukaoniya, ndiponso ku dziko lozungulira mizindayo,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
iwo anamva, nathawira ku midzi ya Lukaoniya, Lustra ndi Derbe, ndi dziko lozungulirapo: