Acts 15:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndidzachita choncho kuti anthu ena onse afunefune Ambuye, ndiye kuti, anthu a mitundu yonse amene amadziŵika ndi dzina langa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kuti anthu otsalira afunefune Ambuye, ndi amitundu onse amene dzina langa linatchulidwa pa iwo,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
kuti anthu otsalawo afunefune Ambuye, ndi anthu onse a mitundu ina amene atchedwa ndi dzina langa, akutero Ambuye, amene amachita zinthu zimenezi
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kuti anthu otsalira afunefune Ambuye, Ndi amitundu onse amene dzina langa linachulidwa pa iwo,