Acts 15:18 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Akutero ndi Chauta amene adaulula zimenezi kuyambira kalekale.’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ati Ambuye, amene azidziwitsa zinthu zonsezo chiyambire dziko lapansi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
zinaululidwa kuyambira kalekale.’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ati Ambuye, amene azidziwitsa zinthu zonsezo ciyambire dzikolapansi.