Acts 15:23 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
kuti akapereke kalata yonena kuti, “Abale, ife atumwi pamodzi ndi akulu a mpingo tikuti moni inu abale a ku Antiokeya, a ku Siriya, ndi a ku Silisiya, amene simuli Ayuda.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Atumwi ndi abale akulu kwa abale a mwa amitundu a m'Antiokeya, ndi Siriya, ndi Silisiya, tikulankhulani:
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
kuti akapereke kalata yonena kuti, Kuchokera kwa atumwi ndi akulu ampingo, abale anu, Kwa anthu a mitundu ina okhulupirira a ku Antiokeya, Siriya ndi Kilikiya: Tikupereka moni.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Atumwi ndi abale akuru kwa abale a mwa amitundu a m'Antiokeya, ndi Suriya, ndi Kilikiya, tikulankhulani: