Acts 15:35 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Paulo ndi Barnabasi adakhalabe ku Antiokeya, akuphunzitsa ndi kulalika mau a Ambuye pamodzi ndi anthu ena ambiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma Paulo ndi Barnabasi anakhalabe m'Antiokeya, nalinkuphunzitsa, ndi kulalikira mau a Ambuye pamodzi ndi ena ambiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Paulo ndi Barnaba anatsalira ku Antiokeya kumene iwo pamodzi ndi ena ambiri anaphunzitsa ndi kulalikira Mawu a Ambuye.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma Paulo ndi Bamaba anakhalabe m'Antiokeya, nalinkuphunzitsa, ndi kulalikira mau a Ambuye pamodzi ndi ena ambiri.