Acts 15:38 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Paulo adaganiza kuti sibwino kumtenganso, chifukwa paja iye adaaŵasiya ku Pamfiliya, osapita nao ku ntchito.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma sikunamkomera Paulo kumtenga iye amene anawasiya nabwerera pa Pamfiliya paja osamuka nao kuntchito.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Paulo anaganiza kuti sichinali cha nzeru kumutenga Yohane chifukwa iye anawathawa ku Pamfiliya ndipo sanapitirire nawo pa ntchito.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma sikunamkomera Paulo kumtenga iye amene anawasiya nabwerera pa Pamfuliya paja osamuka nao kunchito.