Acts 15:40 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Paulo adasankhula Silasi, ndipo abale ataŵapempherera kuti Ambuye aŵadalitse, adanyamuka.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma Paulo anasankha Silasi, namuka, woikizidwa ndi abale ku chisomo cha Ambuye.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Paulo anasankha Sila. Abale atawapempherera kwa Ambuye kuti alandire chisomo, ananyamuka.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma Paulo anasankha Sila, namuka, woikizidwa ndi abale ku cisomo ca Ambuye.