Acts 16:20 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Atafika nawo kwa akulu oweruza milandu, adaŵauza kuti, “Anthu aŵa ndi Ayuda, ndipo akuvutitsa mumzinda mwathu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo pamene adanka nao kwa oweruza, anati, Anthu awa avuta kwambiri mudzi wathu, ndiwo Ayuda,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anawabweretsa iwo kwa oweruza milandu ndipo anati, “Anthu awa ndi Ayuda, iwo akuvutitsa mu mzinda wathu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo pamene adanka nao kwa oweruza, anati, Anthu awa abvuta kwambiri mudzi wathu, ndiwo Ayuda,