Acts 16:22 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu onse adagudukira Paulo ndi Silasi, ndipo akulu oweruza milandu aja adaŵang'ambira zovala zao, nalamula kuti aŵakwapule.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo linagumukira iwo khamulo; ndipo oweruza anawang'ambira malaya ao; nalamulira kuti awakwapule.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Gulu la anthu linatsutsana ndi Paulo ndi Sila, ndipo woweruza milandu analamula kuti avulidwe ndi kumenyedwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo linagumukira iwo khamulo; ndipo oweruza anawang'ambira maraya ao; nalamulira kuti awakwapule.

Recommended Reading