Acts 16:24 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chifukwa cha mau ameneŵa, woyang'anira ndende uja adakaŵatsekera m'chipinda cha m'katikati mwa ndende, namangirira mapazi ao m'matangadza.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakumva iye kulamulira kotero anawaika m'chipinda cha m'kati, namangitsa mapazi ao m'zigologolo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chifukwa cha mawu amenewa woyangʼanira ndende anakawayika mʼchipinda chamʼkati mwa ndende, nawamangirira miyendo yawo mʼzigologolo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakumva iye kulamulira kotero anawaika m'cipinda ca m'kati, namangitsa mapazi ao m'zigologolo.