Acts 16:28 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Paulo adafuula kuti, “Iwe usadzipweteke! Tonse tilipo!”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma Paulo anafuula ndi mau akulu, nati, Usadzipweteka wekha; tonse tili muno.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Paulo anafuwula kuti, “Usadzipweteke! Tonse tilipo!”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma Paulo anapfuula ndi mau akuru, nati, Usadzipweteka wekha; tonse tiri muno.