Acts 16:30 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono adaŵatulutsira kunja, naŵafunsa kuti, “Mabwana, Kodi ndichite chiyani kuti ndipulumuke?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
nawatulutsira iwo kunja, nati, Ambuye, ndichitenji kuti ndipulumuke?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anawatulutsa kunja ndipo anawafunsa kuti, “Amuna inu, ndichite chiyani kuti ndipulumuke?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
nawaturutsira iwo kunja, nati, Ambuye, ndicitenji kuti ndipulumuke?