Acts 16:35 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
M'maŵa kutacha, akulu oweruza milandu adatuma asilikali kukanena kuti, “Amasuleni anthu aja azipita.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kutacha, oweruza anatumiza akapitao, kuti, Mukamasule anthu aja.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kutacha, woweruza milandu uja anatuma asilikali kwa woyangʼanira ndendeyo kukanena kuti, “Amasuleni anthu aja.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kutaca, oweruza anatumiza akapitao, kuti, Mukamasule anthu aja.