Acts 17:20 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pakuti zina zimene mukutiwuzazi nzachilendo, ndipo tikufuna kudziŵa kuti zinthuzi nzotani.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti ufika nazo kumakutu athu zachilendo: tifuna tsono kudziwa, izi zitani?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwe ukubweretsa zinthu zina zachilendo mʼmakutu mwathu, ndipo ife tikufuna tidziwe tanthauzo lake.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti ufika nazo ku makutu athu zacilendo: tifuna tsono kudziwa, izi zitani?