Acts 17:34 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma ena adamtsata, nakhulupirira. Pakati pao panali Dionizio, mmodzi mwa a bwalo la milandu lotchedwa Areopagi, ndiponso mai wina, dzina lake Damalisi, ndi enanso.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma ena anadziphatika kwa iye, nakhulupirira; mwa iwonso munali Dionizio Mwareopagi, ndi mkazi dzina lake Damarisi, ndi ena pamodzi nao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu ena ochepa anamutsatira Paulo ndipo anakhulupirira. Pakati pawo panali Dionisiyo mmodzi wa bwalo la Areopagi ndi mayi wina wotchedwa Damalisi ndi enanso.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma ena anadziphatika kwa iye, nakhulupira; mwa iwonso munali Dionisiyo Mareopagi, ndi mkazi dzina lace Damarisi, ndi ena pamodzi nao.