Acts 17:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mau ameneŵa adautsa mitima ya anthuwo ndi ya akulu amumzinda aja.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anavuta anthu, ndi akulu a mudzi, pamene anamva zimenezi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Atamva zimenezi, gulu la anthu ndi akulu a mzinda anavutika mu mtima.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anabvuta anthu, ndi akuru a mudzi, pamene anamva zimenezi.