Acts 17:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Yasoni ndi anzake aja atalipira mlanduwo, akuluwo adaŵamasula.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo pamene analandira chikole kwa Yasoni ndi enawo, anawamasula.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo analipiritsa Yasoni ndi anzakewo ndipo anawamasula.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo pamene analandira cikole kwa Yasoni ndi enawo, anawamasula.