Acts 18:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
pakuti Ine ndili nawe pamodzi. Palibe munthu adzakukhudza kuti akuchite choipa, ndipo ndili nawo anthu ambiri mumzinda muno.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
chifukwa Ine ndili pamodzi ndi iwe, ndipo palibe munthu adzautsana ndi iwe kuti akuipse; chifukwa ndili nao anthu ambiri m'mudzi muno.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti Ine ndili nawe, palibe aliyense amene adzakukhudza ndi kukuchitira choyipa, chifukwa mu mzinda muno ndili ndi anthu ambiri.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
cifukwa Ine ndiri pamodzi ndi iwe, ndipo palibe munthu adzautsana ndi iwe kuti akuipse; cifukwa ndiri nao anthu ambiri m'mudzi muno.