Acts 18:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iwo adati, “Munthu uyu akukopa anthu kuti azipembedza Mulungu mwa njira zotsutsana ndi Malamulo athu.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kuti, Uyu akopa anthu apembedze Mulungu pokana chilamulo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo anati, “Munthu uyu akukopa anthu kuti azipembedza Mulungu mwanjira zotsutsana ndi malamulo athu.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
kuti, Uyu akopa anthu apembedze Mulungu pokana cilamulo.